Agalatiya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu ana anga,+ ndayambanso kumva kupweteka chifukwa cha inu ngati mayi amene watsala pangʼono kubereka. Ndipitiriza kumva kupweteka kumeneku mpaka mudzayambe kusonyeza makhalidwe a Khristu. 1 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu mukudziwa bwino kuti aliyense wa inu tinkamudandaulira, kumulimbikitsa komanso kumulangiza+ ngati mmene bambo+ amachitira ndi ana ake.
19 Inu ana anga,+ ndayambanso kumva kupweteka chifukwa cha inu ngati mayi amene watsala pangʼono kubereka. Ndipitiriza kumva kupweteka kumeneku mpaka mudzayambe kusonyeza makhalidwe a Khristu.
11 Inu mukudziwa bwino kuti aliyense wa inu tinkamudandaulira, kumulimbikitsa komanso kumulangiza+ ngati mmene bambo+ amachitira ndi ana ake.