2 Akorinto 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nʼchifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi ndili kuno, kuti ndikadzabwera ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu, chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu+ kuti ndizikulimbikitsani, osati kukufooketsani.
10 Nʼchifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi ndili kuno, kuti ndikadzabwera ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu, chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu+ kuti ndizikulimbikitsani, osati kukufooketsani.