2 Akorinto 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho ndife akazembe+ mʼmalo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife. Monga anthu amene akugwira ntchito mʼmalo mwa Khristu tikupempha kuti: “Gwirizananinso ndi Mulungu.”
20 Choncho ndife akazembe+ mʼmalo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife. Monga anthu amene akugwira ntchito mʼmalo mwa Khristu tikupempha kuti: “Gwirizananinso ndi Mulungu.”