Yesaya 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wanena kuti: “Pa nthawi yosonyeza kukoma mtima kwanga, ndinakuyankha.+Ndipo pa tsiku la chipulumutso ndinakuthandiza.+Ndinkakuteteza kuti ndikupereke ngati pangano kwa anthu,+Kuti ndikonzenso dzikolo,Kuti anthuwo atengenso cholowa chawo chimene chinali bwinja,+
8 Yehova wanena kuti: “Pa nthawi yosonyeza kukoma mtima kwanga, ndinakuyankha.+Ndipo pa tsiku la chipulumutso ndinakuthandiza.+Ndinkakuteteza kuti ndikupereke ngati pangano kwa anthu,+Kuti ndikonzenso dzikolo,Kuti anthuwo atengenso cholowa chawo chimene chinali bwinja,+