Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa Mulungu amene amandipatsa mphamvu zimene ndikufunikira.+ Chivumbulutso 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso kuti pali anthu amene amanena kuti ndi Ayuda ndipo amakunyoza. Koma sikuti iwo ndi Ayuda, mʼmalomwake iwo ndi sunagoge wa Satana.+
13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa Mulungu amene amandipatsa mphamvu zimene ndikufunikira.+
9 ‘Ndikudziwa masautso ako ndi umphawi wako, koma ndiwe wolemera.+ Ndikudziwanso kuti pali anthu amene amanena kuti ndi Ayuda ndipo amakunyoza. Koma sikuti iwo ndi Ayuda, mʼmalomwake iwo ndi sunagoge wa Satana.+