Aefeso 5:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho musamachite zimene iwo amachita.* 8 Chifukwa poyamba munali ngati mdima, koma pano muli ngati kuwala+ popeza ndinu ogwirizana ndi Ambuye.+ Pitirizani kuyenda ngati ana a kuwala.
7 Choncho musamachite zimene iwo amachita.* 8 Chifukwa poyamba munali ngati mdima, koma pano muli ngati kuwala+ popeza ndinu ogwirizana ndi Ambuye.+ Pitirizani kuyenda ngati ana a kuwala.