Mateyu 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Chifukwa Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira+ ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+ Chivumbulutso 12:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo kumwamba kunabuka nkhondo: Mikayeli*+ ndi angelo ake anamenyana ndi chinjoka. Chinjokacho ndi angelo ake chinamenya nkhondo, 8 koma sanapambane* ndipo malo awo sanapezekenso kumwamba.
10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Chifukwa Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira+ ndipo uyenera kutumikira iye yekha basi.’”+
7 Ndipo kumwamba kunabuka nkhondo: Mikayeli*+ ndi angelo ake anamenyana ndi chinjoka. Chinjokacho ndi angelo ake chinamenya nkhondo, 8 koma sanapambane* ndipo malo awo sanapezekenso kumwamba.