Afilipi 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 chifukwa ndikudziwa kuti zimenezi zidzachititsa kuti ndipulumutsidwe chifukwa cha mapembedzero anu+ komanso ndi thandizo la mzimu wa Yesu Khristu.+ Filimoni 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso ukonzeretu chipinda choti ndidzafikiremo. Ndikukhulupirira kuti chifukwa cha mapemphero anu, ndimasulidwa kuti ndidzakutumikireni.+
19 chifukwa ndikudziwa kuti zimenezi zidzachititsa kuti ndipulumutsidwe chifukwa cha mapembedzero anu+ komanso ndi thandizo la mzimu wa Yesu Khristu.+
22 Komanso ukonzeretu chipinda choti ndidzafikiremo. Ndikukhulupirira kuti chifukwa cha mapemphero anu, ndimasulidwa kuti ndidzakutumikireni.+