Levitiko 26:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndidzaika chihema changa pakati panu,+ ndipo sindidzakukanani. 12 Ine ndidzayenda pakati panu ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga.+ Ezekieli 37:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tenti yanga idzakhala* pakati pawo.* Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.+
11 Ine ndidzaika chihema changa pakati panu,+ ndipo sindidzakukanani. 12 Ine ndidzayenda pakati panu ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga.+
27 Tenti yanga idzakhala* pakati pawo.* Ine ndidzakhala Mulungu wawo ndipo iwo adzakhala anthu anga.+