-
Yesaya 43:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndidzauza kumpoto kuti, ‘Abwezere kwawo!’+
Ndipo ndidzauza kumʼmwera kuti, ‘Usawakanize.
Bweretsa ana anga aamuna kuchokera kutali komanso ana anga aakazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+
-