2 Akorinto 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndinalimbikitsa Tito kuti abwere kumeneko ndipo ndinamutumiza limodzi ndi mʼbale wina. Titoyo sanakudyereni masuku pamutu ngakhale pangʼono.+ Tinayenda mumzimu umodzi ndipo tinachita zinthu mofanana. Si choncho?
18 Ndinalimbikitsa Tito kuti abwere kumeneko ndipo ndinamutumiza limodzi ndi mʼbale wina. Titoyo sanakudyereni masuku pamutu ngakhale pangʼono.+ Tinayenda mumzimu umodzi ndipo tinachita zinthu mofanana. Si choncho?