Mateyu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yesu anamuuza kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zamumlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti nʼkutsamiritsa mutu wake.”+ Afilipi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ayi sanachite zimenezo, koma anasiya zonse zimene anali nazo nʼkukhala ngati kapolo+ ndipo anakhala munthu.*+
20 Koma Yesu anamuuza kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zamumlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti nʼkutsamiritsa mutu wake.”+
7 Ayi sanachite zimenezo, koma anasiya zonse zimene anali nazo nʼkukhala ngati kapolo+ ndipo anakhala munthu.*+