Aroma 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Abale a ku Makedoniya ndi a ku Akaya apereka mosangalala mphatso kwa oyera ena a ku Yerusalemu omwe ndi osauka.+ 1 Akorinto 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa nkhani ya zopereka zopita kwa oyerawo,+ mukhoza kutsatira malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya. 2 Akorinto 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa utumiki wothandiza anthuwu sikuti ukungothandiza kuti oyerawo apeze zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso kuti anthu ambiri aziyamikira Mulungu mʼmapemphero awo.
26 Abale a ku Makedoniya ndi a ku Akaya apereka mosangalala mphatso kwa oyera ena a ku Yerusalemu omwe ndi osauka.+
16 Pa nkhani ya zopereka zopita kwa oyerawo,+ mukhoza kutsatira malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.
12 Chifukwa utumiki wothandiza anthuwu sikuti ukungothandiza kuti oyerawo apeze zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso kuti anthu ambiri aziyamikira Mulungu mʼmapemphero awo.