Mateyu 11:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Senzani goli langa ndipo lolani kuti ndikuphunzitseni, chifukwa ndine wofatsa ndi wodzichepetsa+ ndipo mudzatsitsimulidwa. 30 Chifukwa goli langa ndi losavuta kunyamula ndipo katundu wanga ndi wopepuka.”
29 Senzani goli langa ndipo lolani kuti ndikuphunzitseni, chifukwa ndine wofatsa ndi wodzichepetsa+ ndipo mudzatsitsimulidwa. 30 Chifukwa goli langa ndi losavuta kunyamula ndipo katundu wanga ndi wopepuka.”