Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tikakumana ndi mayesero,* inuyo mumatonthozedwa ndiponso kupulumutsidwa. Tikatonthozedwa, nanunso mumatonthozedwa ndipo zimenezi zimathandiza kuti mupirire mavuto amene nafenso tikukumana nawo.

  • Akolose 1:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+

  • 1 Atesalonika 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho popeza timakukondani kwambiri,+ tinkafunitsitsa* kukuuzani uthenga wabwino wa Mulungu komanso kupereka miyoyo yathu yeniyeniyo+ kuti tikuthandizeni.

  • Aheberi 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Muzimvera amene akukutsogolerani+ ndipo muziwagonjera+ chifukwa iwo amayangʼanira miyoyo yanu ndipo adzayankha mlandu.+ Muzichita zimenezi kuti azigwira ntchito yawo mosangalala osati modandaula, chifukwa akatero sizingakuyendereni bwino.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena