2 Timoteyo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndikupirirabe zinthu zonse chifukwa cha anthu osankhidwa,+ kuti nawonso alandire chipulumutso kudzera mwa Khristu Yesu komanso alandire ulemerero wosatha.
10 Choncho ndikupirirabe zinthu zonse chifukwa cha anthu osankhidwa,+ kuti nawonso alandire chipulumutso kudzera mwa Khristu Yesu komanso alandire ulemerero wosatha.