Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Pita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa+ chosankhidwa chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina+ komanso kwa mafumu+ ndi Aisiraeli.

  • Machitidwe 26:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma ine ndinati: ‘Ambuye, ndinu ndani kodi?’ Ndipo Ambuye anati: ‘Ndine Yesu amene iwe ukumuzunza. 16 Komabe dzuka ndipo uimirire. Ndaonekera kwa iwe kuti ndikusankhe kuti ukhale mtumiki komanso mboni ya zinthu zonse zokhudza ine, zomwe waona ndiponso zimene ndidzakuonetsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena