Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kudzitama kwanu si kwabwino. Kodi simukudziwa kuti zofufumitsa zapangʼono zimafufumitsa mtanda wonse wa ufa wokandakanda?+

  • 1 Akorinto 15:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Musapusitsidwe.* Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+

  • 2 Timoteyo 2:16-18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma uzipewa nkhani zopeka zimene zimaipitsa zinthu zoyera+ chifukwa zimachititsa kuti anthu ambiri asamaope Mulungu, 17 ndipo mawu awo amafalikira ngati chilonda chonyeka. Ena mwa anthu amenewo ndi Hemenayo ndi Fileto.+ 18 Anthu amenewa akupotoza choonadi, ponena kuti akufa anauka kale+ ndipo akuwononga chikhulupiriro cha ena.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena