Aroma 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa naye+ limodzi pamtengo nʼcholinga chakuti thupi lathu lauchimo likhale lopanda mphamvu,+ kuti tisakhalenso akapolo a uchimo.+
6 Chifukwa tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa naye+ limodzi pamtengo nʼcholinga chakuti thupi lathu lauchimo likhale lopanda mphamvu,+ kuti tisakhalenso akapolo a uchimo.+