1 Atesalonika 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso tikukulimbikitsani abale, kuti muzichenjeza* anthu ochita zosalongosoka,+ muzilankhula molimbikitsa kwa anthu amene ali ndi nkhawa,* muzithandiza ofooka, muzikhala oleza mtima kwa onse.+
14 Komanso tikukulimbikitsani abale, kuti muzichenjeza* anthu ochita zosalongosoka,+ muzilankhula molimbikitsa kwa anthu amene ali ndi nkhawa,* muzithandiza ofooka, muzikhala oleza mtima kwa onse.+