Yohane 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+ Yohane 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikukulamulani kuti muzikondana mofanana ndi mmene ine ndimakukonderani.+ 1 Yohane 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo iye anatipatsa lamulo lakuti, munthu amene amakonda Mulungu azikondanso mʼbale wake.+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+