2 Akorinto 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova* ndi Mzimu+ ndipo pamene pali mzimu wa Yehova,* pali ufulu.+ Agalatiya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu. Choncho khalani olimba+ ndipo musalole kuti mumangidwenso mugoli la ukapolo.+
5 Khristu anatimasula kuti tikhale ndi ufulu umenewu. Choncho khalani olimba+ ndipo musalole kuti mumangidwenso mugoli la ukapolo.+