-
Agalatiya 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma nditaona kuti sankachita zinthu mogwirizana ndi choonadi cha uthenga wabwino,+ ndinauza Kefa* pamaso pa onse kuti: “Ngati iweyo, ngakhale kuti ndiwe Myuda, ukukhala ngati anthu a mitundu ina, osati ngati Ayuda, nʼchifukwa chiyani ukufuna kuchititsa anthu a mitundu ina kuti azitsatira chikhalidwe cha Ayuda?”+
-