Machitidwe 11:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ophunzirawo anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ kwa abale a ku Yudeya, aliyense mogwirizana ndi zimene akanakwanitsa.+ 30 Ndipo anachitadi zimenezo moti thandizolo anapatsira Baranaba ndi Saulo kuti akapereke kwa akulu.+ 1 Akorinto 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa nkhani ya zopereka zopita kwa oyerawo,+ mukhoza kutsatira malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.
29 Choncho ophunzirawo anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ kwa abale a ku Yudeya, aliyense mogwirizana ndi zimene akanakwanitsa.+ 30 Ndipo anachitadi zimenezo moti thandizolo anapatsira Baranaba ndi Saulo kuti akapereke kwa akulu.+
16 Pa nkhani ya zopereka zopita kwa oyerawo,+ mukhoza kutsatira malangizo amene ndinapereka ku mipingo ya ku Galatiya.