Agalatiya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndikukhulupirira kuti inu amene muli ogwirizana ndi Ambuye,+ simudzasintha maganizo. Koma munthu amene amakuvutitsaniyo+ kaya akhale ndani, adzalandira chiweruzo chomuyenerera.
10 Ndikukhulupirira kuti inu amene muli ogwirizana ndi Ambuye,+ simudzasintha maganizo. Koma munthu amene amakuvutitsaniyo+ kaya akhale ndani, adzalandira chiweruzo chomuyenerera.