Machitidwe 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Paulo ataona kuti ena a iwo anali Asaduki ndipo ena anali Afarisi, anafuula mʼkhotimo kuti: “Anthu inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa chifukwa cha chiyembekezo chakuti akufa adzauka.”
6 Paulo ataona kuti ena a iwo anali Asaduki ndipo ena anali Afarisi, anafuula mʼkhotimo kuti: “Anthu inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa chifukwa cha chiyembekezo chakuti akufa adzauka.”