Aefeso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuwonjezera pamenepo, Mulungu anatichititsa kuti tikhale ndi moyo ndipo anatipatsa malo oti tikakhale kumwamba chifukwa anatigwirizanitsa ndi Khristu Yesu.+
6 Kuwonjezera pamenepo, Mulungu anatichititsa kuti tikhale ndi moyo ndipo anatipatsa malo oti tikakhale kumwamba chifukwa anatigwirizanitsa ndi Khristu Yesu.+