Salimo 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo sinthani mmene ndimaganizira+ kuti ndikhale wokhulupirika. Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere* nzeru za nthawi* ino, koma khalani munthu watsopano posintha kwambiri maganizo anu,+ kuti muzindikire chifuniro cha Mulungu,+ chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo sinthani mmene ndimaganizira+ kuti ndikhale wokhulupirika.
2 Musamatengere* nzeru za nthawi* ino, koma khalani munthu watsopano posintha kwambiri maganizo anu,+ kuti muzindikire chifuniro cha Mulungu,+ chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.