-
1 Petulo 3:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Inunso amuna, pitirizani kukhala ndi akazi anu mowadziwa bwino. Muziwapatsa ulemu+ chifukwa akazi ali ngati chiwiya chosachedwa kusweka. Muzichita zimenezi kuti mapemphero anu asatsekerezedwe, chifukwa mudzalandira nawo limodzi moyo umene Mulungu adzakupatseni+ chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu.
-