Aroma 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri, ndife thupi limodzi mwa Khristu ndipo ndife ziwalo zolumikizana.+ Aefeso 1:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu anaikanso zinthu zonse pansi pa mapazi ake,+ ndipo anamuika kuti akhale mutu wa zinthu zonse zimene ndi zokhudzana ndi mpingo+ 23 umene ndi thupi lake+ ndipo ndi wodzaza ndi Khristu, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.
5 Chimodzimodzinso ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri, ndife thupi limodzi mwa Khristu ndipo ndife ziwalo zolumikizana.+
22 Mulungu anaikanso zinthu zonse pansi pa mapazi ake,+ ndipo anamuika kuti akhale mutu wa zinthu zonse zimene ndi zokhudzana ndi mpingo+ 23 umene ndi thupi lake+ ndipo ndi wodzaza ndi Khristu, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.