Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mawu awa amene ndikukulamulani lerowa azikhala pamtima panu, 7 ndipo muziwakhomereza* mumtima mwa ana anu.+ Muzilankhula nawo mawuwo mukakhala pansi mʼnyumba mwanu, mukamayenda pamsewu, mukamagona komanso mukadzuka.+

  • Miyambo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mwana wanga, usakane malangizo* a Yehova+

      Ndipo usanyansidwe ndi kudzudzula kwake,+

  • Miyambo 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Langa mwana wako padakali chiyembekezo,+

      Ndipo usakhale ndi mlandu wochititsa* kuti afe.+

  • Miyambo 22:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Phunzitsa mwana kuti aziyenda mʼnjira imene akuyenera kuyendamo.+

      Ngakhale akadzakalamba sadzachoka mʼnjira imeneyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena