Agalatiya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa kudulidwa kapena kusadulidwa nʼkosafunika,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+
15 Chifukwa kudulidwa kapena kusadulidwa nʼkosafunika,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+