Aroma 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo kuonedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene wakusonyeza powamasula ndi dipo lolipiridwa ndi Khristu Yesu,+ kuli ngati mphatso yaulere.+
24 Ndipo kuonedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene wakusonyeza powamasula ndi dipo lolipiridwa ndi Khristu Yesu,+ kuli ngati mphatso yaulere.+