Maliko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+
24 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, zinthu zonse zimene mukupempha ndi kuzipempherera, muzikhulupirira kuti mwazilandira kale ndipo mudzazilandiradi.+