Akolose 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuti ndikwanitse kuchita zimenezi, ndikugwira ntchito mwakhama ndipo ndikuyesetsa kwambiri podalira mphamvu zake zimene zikugwira ntchito mwamphamvu mwa ine.+
29 Kuti ndikwanitse kuchita zimenezi, ndikugwira ntchito mwakhama ndipo ndikuyesetsa kwambiri podalira mphamvu zake zimene zikugwira ntchito mwamphamvu mwa ine.+