Afilipi 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma panopa ndikuona kuti ndi bwino kuti ndikutumizireni Epafurodito. Ameneyu ndi mʼbale wanga, wantchito mnzanga ndi msilikali mnzanga. Iye ndi nthumwi yanu komanso amanditumikira pa zosowa zanga.+
25 Koma panopa ndikuona kuti ndi bwino kuti ndikutumizireni Epafurodito. Ameneyu ndi mʼbale wanga, wantchito mnzanga ndi msilikali mnzanga. Iye ndi nthumwi yanu komanso amanditumikira pa zosowa zanga.+