2 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Panopa andisungira chisoti chachifumu cha olungama.+ Ambuye, woweruza wachilungamo,+ adzandipatsa mphotoyi pa tsikulo.+ Sikuti adzapatsa ine ndekha, koma adzapatsanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere. Aheberi 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho, popeza tazunguliridwa ndi gulu lalikulu chonchi la mboni,* tiyeninso titaye cholemera chilichonse ndi tchimo limene limatikola mosavuta.+ Ndipo tithamange mopirira mpikisano umene talowawu.+
8 Panopa andisungira chisoti chachifumu cha olungama.+ Ambuye, woweruza wachilungamo,+ adzandipatsa mphotoyi pa tsikulo.+ Sikuti adzapatsa ine ndekha, koma adzapatsanso onse amene akhala akuyembekezera kuti iye adzaonekere.
12 Choncho, popeza tazunguliridwa ndi gulu lalikulu chonchi la mboni,* tiyeninso titaye cholemera chilichonse ndi tchimo limene limatikola mosavuta.+ Ndipo tithamange mopirira mpikisano umene talowawu.+