Salimo 69:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mayina awo afufutidwe mʼbuku la anthu amoyo,*+Ndipo iwo asalembedwe mʼbuku limene muli mayina a anthu olungama.+ Luka 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komano musasangalale chifukwa choti mizimu yakugonjerani, koma sangalalani chifukwa mayina anu alembedwa kumwamba.”+
28 Mayina awo afufutidwe mʼbuku la anthu amoyo,*+Ndipo iwo asalembedwe mʼbuku limene muli mayina a anthu olungama.+
20 Komano musasangalale chifukwa choti mizimu yakugonjerani, koma sangalalani chifukwa mayina anu alembedwa kumwamba.”+