Aefeso 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chidani chachikulu,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata, mawu achipongwe+ komanso zinthu zonse zoipa zichotsedwe mwa inu.+
31 Chidani chachikulu,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata, mawu achipongwe+ komanso zinthu zonse zoipa zichotsedwe mwa inu.+