Miyambo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wanga, uzitsatira malamulo a bambo ako,Ndipo usasiye kutsatira malangizo* a mayi ako.+ Luka 2:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Kenako ananyamuka nawo limodzi nʼkubwerera ku Nazareti ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+ Aefeso 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana inu, muzimvera makolo anu+ mogwirizana ndi zimene Ambuye amafuna, chifukwa kuchita zimenezi nʼkoyenera.
51 Kenako ananyamuka nawo limodzi nʼkubwerera ku Nazareti ndipo anapitiriza kuwamvera.+ Apanso mayi akewo anasunga mosamala kwambiri mawu onsewa mumtima mwawo.+
6 Ana inu, muzimvera makolo anu+ mogwirizana ndi zimene Ambuye amafuna, chifukwa kuchita zimenezi nʼkoyenera.