Luka 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse komanso kuti asamataye mtima.+ Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani chifukwa cha chiyembekezo. Muzipirira mavuto.+ Muzilimbikira kupemphera.+ Aefeso 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene mukuchita zimenezi, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ pogwiritsa ntchito pemphero+ ndi pembedzero la mtundu uliwonse. Kuti muchite zimenezi khalani maso ndipo nthawi zonse muzipemphera mopembedzera mʼmalo mwa oyera onse.
18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse komanso kuti asamataye mtima.+
18 Pamene mukuchita zimenezi, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ pogwiritsa ntchito pemphero+ ndi pembedzero la mtundu uliwonse. Kuti muchite zimenezi khalani maso ndipo nthawi zonse muzipemphera mopembedzera mʼmalo mwa oyera onse.