Filimoni 23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Epafura,+ mkaidi mnzanga mwa Khristu Yesu, akupereka moni. 24 Maliko, Arisitako,+ Dema+ ndi Luka,+ omwe ndi antchito anzanga, akuperekanso moni.
23 Epafura,+ mkaidi mnzanga mwa Khristu Yesu, akupereka moni. 24 Maliko, Arisitako,+ Dema+ ndi Luka,+ omwe ndi antchito anzanga, akuperekanso moni.