Aefeso 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu.+ 1 Atesalonika 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzithokoza pa chilichonse.+ Mulungu akufuna kuti muzichita zimenezi chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu.
20 Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu.+
18 Muzithokoza pa chilichonse.+ Mulungu akufuna kuti muzichita zimenezi chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu.