Aroma 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amadya chilichonse, asamanyoze amene sadya, ndipo wosadyayo asamaweruze amene amadya chilichonse,+ popeza iye analandiridwa ndi Mulungu. Aroma 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa pa nkhani ya Ufumu wa Mulungu chofunika kwambiri si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo, mtendere ndi chimwemwe zimene zimabwera ndi mzimu woyera.
3 Amene amadya chilichonse, asamanyoze amene sadya, ndipo wosadyayo asamaweruze amene amadya chilichonse,+ popeza iye analandiridwa ndi Mulungu.
17 Chifukwa pa nkhani ya Ufumu wa Mulungu chofunika kwambiri si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo, mtendere ndi chimwemwe zimene zimabwera ndi mzimu woyera.