Agalatiya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nʼchimodzimodzinso ifeyo. Pamene tinali ana, tinali akapolo chifukwa tinkayendera mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera.*+ Akolose 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani kuti wina asakugwireni ukapolo,* pogwiritsa ntchito nzeru za anthu ndi chinyengo chopanda pake,+ mogwirizana ndi miyambo ya anthu komanso mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera, osati mogwirizana ndi Khristu,
3 Nʼchimodzimodzinso ifeyo. Pamene tinali ana, tinali akapolo chifukwa tinkayendera mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera.*+
8 Samalani kuti wina asakugwireni ukapolo,* pogwiritsa ntchito nzeru za anthu ndi chinyengo chopanda pake,+ mogwirizana ndi miyambo ya anthu komanso mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera, osati mogwirizana ndi Khristu,