Aefeso 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munaphunzitsidwa kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi makhalidwe anu akale, umenenso ukuipitsidwa chifukwa cha zilakolako zachinyengo za umunthuwo.+
22 Munaphunzitsidwa kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi makhalidwe anu akale, umenenso ukuipitsidwa chifukwa cha zilakolako zachinyengo za umunthuwo.+