Machitidwe 17:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako iwo anayenda kudutsa ku Amfipoli ndi ku Apoloniya ndipo anafika ku Tesalonika,+ kumene kunali sunagoge wa Ayuda. 2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa mʼsunagogemo ndipo kwa milungu itatu anakambirana nawo mfundo za mʼMalemba.+
17 Kenako iwo anayenda kudutsa ku Amfipoli ndi ku Apoloniya ndipo anafika ku Tesalonika,+ kumene kunali sunagoge wa Ayuda. 2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa mʼsunagogemo ndipo kwa milungu itatu anakambirana nawo mfundo za mʼMalemba.+