Miyambo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Koma Yehova ndi amene amayesa mitima.+ Yeremiya 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amaweruza mwachilungamo.Amafufuza maganizo* komanso mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,Chifukwa mlandu wanga ndausiya mʼmanja mwanu.
3 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Koma Yehova ndi amene amayesa mitima.+
20 Koma Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amaweruza mwachilungamo.Amafufuza maganizo* komanso mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango,Chifukwa mlandu wanga ndausiya mʼmanja mwanu.