Mateyu 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Woyesayo+ anabwera nʼkumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, uzani miyalayi kuti isanduke mitanda ya mkate.” 2 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mofanana ndi mmene njoka inanamizira Hava ndi chinyengo chake,+ nkhawa yanga ndi yakuti mwina maganizo anunso angapotozedwe moti simungakhalenso oona mtima ndiponso oyera. Koma munthu wa Khristu amafunika kukhala woona mtima komanso woyera.+
3 Ndiyeno Woyesayo+ anabwera nʼkumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, uzani miyalayi kuti isanduke mitanda ya mkate.”
3 Mofanana ndi mmene njoka inanamizira Hava ndi chinyengo chake,+ nkhawa yanga ndi yakuti mwina maganizo anunso angapotozedwe moti simungakhalenso oona mtima ndiponso oyera. Koma munthu wa Khristu amafunika kukhala woona mtima komanso woyera.+