2 Atesalonika 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho ifeyo timanyadira+ tikamanena za inu ku mipingo ya Mulungu chifukwa cha kupirira kwanu ndi chikhulupiriro chimene mumasonyeza mukamazunzidwa komanso kulimbana ndi mavuto* amene mukukumana nawo.*+
4 Choncho ifeyo timanyadira+ tikamanena za inu ku mipingo ya Mulungu chifukwa cha kupirira kwanu ndi chikhulupiriro chimene mumasonyeza mukamazunzidwa komanso kulimbana ndi mavuto* amene mukukumana nawo.*+